Clement Gweza says

Clement Gweza – Mphunzitsi

Kwa ine ndikungoyamikira ntchito yanu yokhudzana ndi miyoyo ya anthu omwe ali ndi ulubino, makamaka pa zovuta zomwe tikukumana nazo ngakhale zogwira mtima, ndikuyembekeza kuti bukuli liwatsogolere. Kusintha kwakukulu pamoyo wathu wa albinos chifukwa anthu amafunika kudziwa ndi kutithandiza kuthetsa mavuto ena omwe tikukumana nawo, mwachitsanzo: mavuto a zaumoyo, maphunziro, tsankho ndi kuzunzidwa, kuphatikizapo umphawi!
Zikomo kawambini  anzanga nonse aku Italy

Clement Gweza – Teacher​

For me it's just a small sign of appreciation for your project concerning the life of people with albinism; in particular on the challenges we are facing successfully. This is what I hope the book will bring: a big change in the life of us albinos, because people must be aware and must know how to help us solve some of the problems we are facing, for example: health challenges, education, discrimination and persecution, to say nothing about poverty!​

Many thanks to all our Italian friends.​